2 Mbiri 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lamkuwa.+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.+
4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lamkuwa.+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 m’litali, mikono 20 m’lifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.+