Levitiko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+ Levitiko 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kumeneko akulu a khamu la Isiraeli aziika manja awo pamutu wa ng’ombeyo+ pamaso pa Yehova, ndipo aziipha pamaso pa Yehova.
4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+
15 Kumeneko akulu a khamu la Isiraeli aziika manja awo pamutu wa ng’ombeyo+ pamaso pa Yehova, ndipo aziipha pamaso pa Yehova.