Salimo 68:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+ Salimo 89:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene amafuula mosangalala.+Iwo amayendabe m’kuwala kwa nkhope yanu, inu Yehova.+
25 Oimba nyimbo anali patsogolo, oimba zoimbira za zingwe anali pambuyo pawo,+Pakati panali atsikana akuimba maseche.+