-
1 Mbiri 29:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Anthuwo anayamba kupereka nsembe+ kwa Yehova, ndipo anali kupereka nsembe zopsereza+ kwa Yehova mpaka tsiku lotsatira. Anapereka ng’ombe zamphongo zazing’ono 1,000, nkhosa zamphongo 1,000, ana a nkhosa amphongo 1,000, ndi nsembe zake zachakumwa.+ Iwo anapereka nsembe zambirimbiri za Isiraeli yense.+
-