Ekisodo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uzani khamu lonse la Isiraeli kuti, ‘Pa tsiku la 10 la mwezi uno mabanja onse ochokera mwa kholo limodzi atenge nkhosa imodziimodzi,+ banja lililonse litenge nkhosa imodzi. 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+
3 Uzani khamu lonse la Isiraeli kuti, ‘Pa tsiku la 10 la mwezi uno mabanja onse ochokera mwa kholo limodzi atenge nkhosa imodziimodzi,+ banja lililonse litenge nkhosa imodzi.
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+