2 Mbiri 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ansembe anatuluka m’malo oyera (chifukwa ansembe onse amene analipo anali atadziyeretsa+ ndipo panalibe chifukwa choti atumikire motsatira magulu awo).+ 2 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo anasonkhanitsa abale awo pamodzi n’kudziyeretsa.+ Ndiyeno anabwera kudzayeretsa+ nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu+ a Yehova.
11 Tsopano ansembe anatuluka m’malo oyera (chifukwa ansembe onse amene analipo anali atadziyeretsa+ ndipo panalibe chifukwa choti atumikire motsatira magulu awo).+
15 Iwo anasonkhanitsa abale awo pamodzi n’kudziyeretsa.+ Ndiyeno anabwera kudzayeretsa+ nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu+ a Yehova.