Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.

  • 2 Mbiri 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino+ zimene Yehova anachitira Davide, Solomo, ndiponso zimene anachitira anthu ake Aisiraeli.+

  • Nehemiya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nehemiya anapitiriza kunena kuti: “Pitani mukadye zinthu zonona, kumwa zinthu zokoma ndi kugawa chakudya+ kwa anthu amene sanathe kudzikonzera chakudya, pakuti lero ndi tsiku lopatulika kwa Ambuye wathu. Choncho musadzimvere chisoni pakuti chimwemwe chimene Yehova amapereka ndicho malo anu achitetezo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena