2 Mbiri 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ansembe anazipha n’kuzipereka nsembe yamachimo pamodzi ndi magazi ake paguwa lansembe kuti aphimbe machimo a Aisiraeli onse,+ popeza mfumu inati nsembe yopsereza ndi yamachimoyo+ ikhale ya Aisiraeli onse.+
24 Tsopano ansembe anazipha n’kuzipereka nsembe yamachimo pamodzi ndi magazi ake paguwa lansembe kuti aphimbe machimo a Aisiraeli onse,+ popeza mfumu inati nsembe yopsereza ndi yamachimoyo+ ikhale ya Aisiraeli onse.+