2 Mbiri 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anaika akuluakulu a asilikali+ kuti aziyang’anira anthuwo, ndipo anawauza kuti akumane naye pabwalo+ la mzindawo limene linali pachipata. Kumeneko iye anawalankhula mowalimbitsa mtima+ kuti:
6 Kenako anaika akuluakulu a asilikali+ kuti aziyang’anira anthuwo, ndipo anawauza kuti akumane naye pabwalo+ la mzindawo limene linali pachipata. Kumeneko iye anawalankhula mowalimbitsa mtima+ kuti: