Salimo 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu ndi Mfumu ya dziko lonse lapansi.+Imbani nyimbo zotamanda ndi kuchita zinthu mozindikira.+ Miyambo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu adzatamandidwa chifukwa cha pakamwa pake panzeru,+ koma wa mtima wopotoka adzanyozedwa.+
7 Pakuti Mulungu ndi Mfumu ya dziko lonse lapansi.+Imbani nyimbo zotamanda ndi kuchita zinthu mozindikira.+