Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere: Deuteronomo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+
8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+