Nehemiya 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe, mwana wamwamuna wa Aroni, azikhala ndi Alevi pamene iwo akulandira chakhumi.* Aleviwo azipereka gawo limodzi mwa magawo 10 a chakhumicho kunyumba ya Mulungu+ wathu kuzipinda zodyera+ m’nyumba yosungiramo zinthu.
38 Wansembe, mwana wamwamuna wa Aroni, azikhala ndi Alevi pamene iwo akulandira chakhumi.* Aleviwo azipereka gawo limodzi mwa magawo 10 a chakhumicho kunyumba ya Mulungu+ wathu kuzipinda zodyera+ m’nyumba yosungiramo zinthu.