Levitiko 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Chakhumi* chilichonse+ cha zinthu za m’dzikolo, kaya ndi zokolola m’munda kapena zipatso za m’mitengo, ndi cha Yehova. Chakhumi chimenechi ndi chopatulika kwa Yehova. Deuteronomo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kumapeto kwa zaka zitatu uzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zako zonse m’chaka chimenecho,+ ndipo uzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.
30 “‘Chakhumi* chilichonse+ cha zinthu za m’dzikolo, kaya ndi zokolola m’munda kapena zipatso za m’mitengo, ndi cha Yehova. Chakhumi chimenechi ndi chopatulika kwa Yehova.
28 “Kumapeto kwa zaka zitatu uzidzabweretsa chakhumi cha zokolola zako zonse m’chaka chimenecho,+ ndipo uzidzachisiya mkati mwa mzinda wanu.