2 Samueli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu. 2 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira.+
18 Davide atamaliza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, anadalitsa+ anthu m’dzina la Yehova+ wa makamu.
3 Kenako mfumu inatembenuka n’kuyang’ana anthuwo. Ndiyeno inayamba kudalitsa+ mpingo wonse wa Isiraeli. Pamenepo n’kuti mpingo wonse wa Isiraeli utaimirira.+