2 Mbiri 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Komanso, nsembe zopsereza+ ndiponso mafuta+ a nsembe zachiyanjano+ zinali zambiri. Nazonso nsembe zachakumwa+ zimene zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zopserezazo zinali zambiri. Chotero utumiki wa panyumba ya Yehova unakonzedwa.+
35 Komanso, nsembe zopsereza+ ndiponso mafuta+ a nsembe zachiyanjano+ zinali zambiri. Nazonso nsembe zachakumwa+ zimene zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zopserezazo zinali zambiri. Chotero utumiki wa panyumba ya Yehova unakonzedwa.+