12 Pa nthawi imeneyo, Berodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata+ ndi mphatso kwa Hezekiya chifukwa anamva kuti Hezekiya anali kudwala.
39Pa nthawi imeneyo, Merodaki-baladani+ mwana wa Baladani mfumu ya Babulo,+ anatumiza makalata ndi mphatso+ kwa Hezekiya atamva kuti iye anadwala koma tsopano wapezanso mphamvu.+