2 Mafumu 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanga maguwa ansembe m’nyumba ya Yehova,+ imene ponena za iyo Yehova anati: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+ 2 Mafumu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ m’mabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+
4 Anamanga maguwa ansembe m’nyumba ya Yehova,+ imene ponena za iyo Yehova anati: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+
5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ m’mabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+