1 Mafumu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.