2 Mafumu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pomaliza pake, atumiki a mfumu Amoni anam’chitira chiwembu n’kumupha+ m’nyumba mwake momwe. Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+