2 Mafumu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yosiya anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira zonse za Davide kholo lake.+ Iye sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
2 Yosiya anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira zonse za Davide kholo lake.+ Iye sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+