2 Mbiri 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komabe anthu anali kuperekabe nsembe m’malo okwezeka,+ kungoti anali kuzipereka kwa Yehova Mulungu wawo.
17 Komabe anthu anali kuperekabe nsembe m’malo okwezeka,+ kungoti anali kuzipereka kwa Yehova Mulungu wawo.