Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 10:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehu atangomaliza kupereka nsembe yopserezayo, nthawi yomweyo anauza asilikali ake othamanga ndi othandiza pamagaleta kuti: “Lowani, apheni! Pasapezeke ndi mmodzi yemwe wotuluka panja.”+ Atamva zimenezi, asilikali ake othamanga ndi othandiza pamagaleta+ aja anayamba kupha anthuwo ndi lupanga n’kumaponyera mitembo yawo panja. Anakafika mpaka m’chipinda chamkati mwa kachisiyo chotchedwa mzinda wa Baala.

  • 2 Mafumu 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kuwonjezera apo, mfumuyo inatulutsa mzati wopatulika+ umene unali m’nyumba ya Yehova, ndipo inapita nawo kuchigwa* cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu n’kukautentha+ kuchigwacho. Itatero, inauperapera n’kuwaza fumbi lake pamanda+ a ana a anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena