Deuteronomo 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+
21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+