Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amuna amene ankapatsidwa ndalama kuti azipereke kwa anthu ogwira ntchito,+ sankafunsidwa+ mmene ayendetsera ndalamazo chifukwa ankagwira ntchito mokhulupirika.+

  • Nehemiya 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Zitatero ndinaika Haneni+ m’bale wanga ndi Hananiya kalonga wa m’Nyumba ya Chitetezo Champhamvu,+ kuti aziyang’anira Yerusalemu. Hananiya anali munthu wodalirika+ ndipo anali woopa kwambiri+ Mulungu woona kuposa anthu ena ambiri.

  • Miyambo 28:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+

  • 1 Akorinto 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena