1 Mbiri 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari. 1 Mbiri 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ana a Merari+ anali Mali+ ndi Musi.+ Pa ana a Yaaziya panali Beno.
6 Ndiyeno Davide anawagawa m’magulu+ ndi kuwapereka kwa ana a Levi.+ Anawapereka kwa Gerisoni, Kohati, ndi Merari.