1 Mbiri 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ena mwa ana a Akohati, abale awo, anali oyang’anira mikate yosanjikiza,+ kuti aziikonza sabata ndi sabata.+ 2 Mbiri 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Alevi+ omwe anali ana a Kohati+ ndi ana a Kora+ anaimirira ndi kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+
32 Ena mwa ana a Akohati, abale awo, anali oyang’anira mikate yosanjikiza,+ kuti aziikonza sabata ndi sabata.+
19 Kenako Alevi+ omwe anali ana a Kohati+ ndi ana a Kora+ anaimirira ndi kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+