Deuteronomo 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+ Salimo 119:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Komanso ndidzanena za zikumbutso zanu pamaso pa mafumu,+Ndipo sindidzachita manyazi.+
19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+