Salimo 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Ndipo odzimvera chisoni mumtima mwawo amawapulumutsa.+
18 Yehova ali pafupi ndi anthu a mtima wosweka.+Ndipo odzimvera chisoni mumtima mwawo amawapulumutsa.+