2 Mbiri 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumuyo itangomva mawu a chilamulowo, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake.+