Machitidwe 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anayendayenda m’madera akumeneko ndi kulimbikitsa ophunzira ndi mawu ambiri,+ kenako anafika ku Girisi. Aheberi 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+ 1 Petulo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+
2 Iye anayendayenda m’madera akumeneko ndi kulimbikitsa ophunzira ndi mawu ambiri,+ kenako anafika ku Girisi.
25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+
12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+