1 Mafumu 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo. 2 Mbiri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova kumalo ake, kuchipinda chamkati+ cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa,+ ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+
38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo.
7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova kumalo ake, kuchipinda chamkati+ cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa,+ ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+