Salimo 135:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu amene mukuimirira m’nyumba ya Yehova,+M’mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.+