Ekisodo 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Usiku umenewu ndi wofunika kuukumbukira polemekeza Yehova, chifukwa anawatulutsa m’dziko la Iguputo. Yehova anafuna kuti ana a Isiraeli onse, m’mibadwo yawo yonse, azikumbukira usiku umenewu.+
42 Usiku umenewu ndi wofunika kuukumbukira polemekeza Yehova, chifukwa anawatulutsa m’dziko la Iguputo. Yehova anafuna kuti ana a Isiraeli onse, m’mibadwo yawo yonse, azikumbukira usiku umenewu.+