Ezara 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anaika ansembe ndi Alevi m’magulu awo+ kuti azichita utumiki wa Mulungu ku Yerusalemu, mogwirizana ndi malangizo a m’buku la Mose.+
18 Kenako anaika ansembe ndi Alevi m’magulu awo+ kuti azichita utumiki wa Mulungu ku Yerusalemu, mogwirizana ndi malangizo a m’buku la Mose.+