Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.

  • 2 Mbiri 29:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwo anapha+ ng’ombezo ndipo ansembe anatenga magazi+ ake n’kuwaza+ paguwa lansembe. Kenako anapha nkhosa zamphongo+ zija n’kuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja n’kuwaza magazi+ ake paguwa lansembe.

  • 2 Mbiri 30:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iwo anaimirira+ m’malo mwawo mogwirizana ndi zimene analamulidwa, malinga ndi lamulo la Mose munthu wa Mulungu woona. Ansembe+ anali kuwaza paguwa lansembe magazi amene anali kulandira kwa Alevi.

  • Aheberi 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo anawazanso magazi aja pachihema+ ndi paziwiya zonse zogwiritsa ntchito potumikira ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena