1 Mbiri 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yahati anali mtsogoleri wawo, ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anakhala nyumba imodzi ya makolo+ ndiponso gulu limodzi lokhala ndi udindo wofanana. 1 Mbiri 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ana a Musi anali Mali,+ Ederi, ndi Yerimoti.+ Amenewa anali ana a Alevi potsata nyumba za makolo awo.+
11 Yahati anali mtsogoleri wawo, ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anakhala nyumba imodzi ya makolo+ ndiponso gulu limodzi lokhala ndi udindo wofanana.
30 Ana a Musi anali Mali,+ Ederi, ndi Yerimoti.+ Amenewa anali ana a Alevi potsata nyumba za makolo awo.+