Levitiko 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo pansembe yachiyanjanoyo azitengapo mafuta ake ndi kuwapereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto.+ Azichotsa mchira wonse wamafuta+ pafupi ndi fupa la msana ndiponso mafuta okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+ Levitiko 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo pambuziyo azitengapo mafuta okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo,+ ndi kuwapereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto.
9 Ndipo pansembe yachiyanjanoyo azitengapo mafuta ake ndi kuwapereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto.+ Azichotsa mchira wonse wamafuta+ pafupi ndi fupa la msana ndiponso mafuta okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+
14 Ndipo pambuziyo azitengapo mafuta okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo,+ ndi kuwapereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto.