1 Mbiri 16:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani+ ndi Yedutuni ndiponso amuna onse amene anasankhidwa+ mwa kutchulidwa mayina kuti aziyamika Yehova,+ chifukwa “kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+
41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani+ ndi Yedutuni ndiponso amuna onse amene anasankhidwa+ mwa kutchulidwa mayina kuti aziyamika Yehova,+ chifukwa “kukoma mtima kwake kosatha kudzakhala mpaka kalekale.”+