42 Anasiya Hemani+ ndi Yedutuni+ limodzi ndi amuna aja kuti aziimba malipenga,+ zinganga ndi zipangizo zina zoimbira nyimbo ya Mulungu woona, ndipo ana+ a Yedutuni anali alonda a pachipata.
3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya,+ Zeri,+ Yesaiya,+ Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya,+ ana 6. Iwowa anali kuyang’aniridwa ndi Yedutuni bambo wawo, amene anali kulosera ndi zeze poyamika ndi potamanda Yehova.+