Ekisodo 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chotero Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Lamulo la pasika ndi ili:+ Mlendo* asadye nawo.+ Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+
16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+