2 Mafumu 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli. 2 Mafumu 23:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iye anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene makolo ake akale anachita.+
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.
32 Iye anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene makolo ake akale anachita.+