1 Mafumu 8:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli, ndi pempho lopempha chifundo, anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova popeza nthawi yonseyi anali chogwada,+ manja ake atawatambasulira kumwamba.+ Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Machitidwe 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Atanena zimenezi, anagwada+ nawo pansi onsewo ndi kupemphera.
54 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli, ndi pempho lopempha chifundo, anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova popeza nthawi yonseyi anali chogwada,+ manja ake atawatambasulira kumwamba.+