2 Samueli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+ Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+
25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+
49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+