Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+ 1 Mbiri 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwana wake wamkazi anali Seera, ndipo iye anamanga mzinda wa Beti-horoni,+ wakumunsi+ ndi wakumtunda.+ Anamanganso mzinda wa Uzeni-seera.
5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+
24 Mwana wake wamkazi anali Seera, ndipo iye anamanga mzinda wa Beti-horoni,+ wakumunsi+ ndi wakumtunda.+ Anamanganso mzinda wa Uzeni-seera.