1 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena a iwo anali amuna osankhidwa kuti aziyang’anira ziwiya zina, ziwiya zonse zopatulika,+ ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ ndi mafuta a basamu.+ 1 Mbiri 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbali ya Alevi, Ahiya anali kuyang’anira chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+
29 Ena a iwo anali amuna osankhidwa kuti aziyang’anira ziwiya zina, ziwiya zonse zopatulika,+ ufa wosalala,+ vinyo,+ mafuta,+ lubani,*+ ndi mafuta a basamu.+
20 Kumbali ya Alevi, Ahiya anali kuyang’anira chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+