1 Mafumu 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.
40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.