1 Mafumu 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pomalizira pake, Rehobowamu anagona ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama Muamoni.+ Kenako Abiyamu+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira m’malo mwake.
31 Pomalizira pake, Rehobowamu anagona ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama Muamoni.+ Kenako Abiyamu+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira m’malo mwake.