1 Mafumu 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’chaka cha 18 cha Mfumu Yerobowamu+ mwana wa Nebati,+ Abiyamu anakhala mfumu ya Yuda.+