1 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu pankachitika nkhondo masiku onse a moyo wa Rehobowamu.+