1 Mafumu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+ 2 Mbiri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+
20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, nthawi yomweyo anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatula fuko la Yuda lokha.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene anali kuyang’anira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma ana a Isiraeli anam’ponya miyala+ n’kumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inakwanitsa kukwera galeta lake n’kuthawira ku Yerusalemu.+